Tiyankhuleni
Yankhulani nafe
Kodi mulindi funso lomwe mukufuna kufunsa pa uthenga omwe mwamvera? Kapena mukufuna thandizo la mapemphero apadela? Muli ndi ndemanga pa zomwe mwamvera? Kodi muli ndi umboni pa zomwe Mtumiki Twaibu anakuthangatani ndipo Mulungu anayankha ndipo mukufuna kugawana ndi ena? Kapena muli ndi dandaulo pa zauthenga omwe mwamvera? Nkuthekanso mwina muli ndi maganizo ena ake othandiza kwa Mtumiki Twaibu, muli olandilidwa kuyankhula nafe kudzela munjila zotsatilazi.
info@umboniwanga.com
mafunso@umboniwanga.com
twaibu@umboniwanga.com
+265 99204 0525
+265 88203 6003